Global Football (Soccer) Event·2 mwa 15

Where You Belong

On the field, there is nothing more important than the ball. The players will do everything to protect it and get the ball where it belongs. In the Game of Life, where do you belong?

Funsani lanu

Mawu a Baibulo

Gawani
Psalm 86:15

But You, O Lord, are a compassionate and gracious God, slow to anger, abounding in loving devotion and faithfulness.

Berean Standard Bible

Public Domain

Werengani zambiri...
Zothandizira Zaulere

Mukufuna kumvetsa Baibulo mozama?

Lowani nawo phunziro lathu la Baibulo

Lembalo la mawu

Chichewa (Chicheŵa)
Mpira nthawi zambili umapangidwa ndi chikopa, mphira ndi kusoka. Siwapadera-dera. Pali miyanda miyanda ya iwo m’dziko lirilonse la dziko lapansi. Koma ukakhala mu bwalo la masewera... sipamakhalanso chofunikira koposa. Wosewera aliyenso mubwalomo amafunitsitsa kudziwa kuti uli pati. Aliyense kumasitandi akukuwa mwa chisangalalo. Miyoyo yao itayiwalidwa, zonse chifukwa cha mpira uwu. Pamene wosewera wapetenga mpira, chidwi chake chimakhala chosayimitsika. Kwa iwo, mu mphindi iyi, palibenso kena kalikonse, ndipo palibe wina aliyense, wofunikira zedi. Sasamala kuti zimatengera mphamvu zochuluka bwanji, kapena kuti angavulale patsogolo pake. Amayimitsa mpira ndi matupi awo omwe. Pali chinthu chimodzi chokha choyenera kuchita... ...kuponyera mpira kumene uyenere kupita. Chimene chingakudabwitseni ndi ichi... Umu ndi mmene Yesu amakuonerani. Yesu amadziwa zonse za inu. Ndipo amakulandirani mulimonsemo, ndipo amafuna kukutetezani ndi kukusamalirani. Yesu anaperekanso moyo wake pa chinthu chimodzi, cholinga chamuyaya... kuti mutha kukhala komwe muyenelera... ku Nyumba. Ndi Iye. Komwe muyenera kukhala. Mpira ukatha, aliyense amachokamo mu sitediyamu. Koma Yesu amakhala akudikilirabe. Inuyo. Yesu amakukondani. Ndi chisankho chanu. Muloleni akubweretseni kunyumba.
JesusFilm